Macitidwe 2:41-44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

41. Pamenepo iwo amene analandira mau ace anabatizidwa; ndipo anaonjezedwa tsiku lomwelo anthu ngati zikwi zitatu.

42. Ndipo 4 anali cikhalire m'ciphunzitso ca atumwi ndi m'ciyanjano, m'kunyema mkate ndi mapemphero.

43. Koma panadza mantha pa anthu onse; ndipo 5 zozizwa ndi zizindikilo zambiri zinacitika ndi atumwi.

44. Ndipo onse akukhulupira anali pamodzi, 6 nakhala nazo zonse zodyerana.

Macitidwe 2