Macitidwe 2:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndi mau ena ambiri anacita umboni, nawadandaulira iwo, nanena, Mudzipulumutse kwa mbadwo uno wokhotakhota.

Macitidwe 2

Macitidwe 2:38-45