Macitidwe 2:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Petro anati kwa iwo, Lapani, batizidwani yense wa inu m'dzina la Yesu Kristu kuloza ku cikhululukiro ca macimo anu; ndipo mudzalandira mphatso ya Mzimu Woyera.

Macitidwe 2

Macitidwe 2:36-40