Macitidwe 2:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero, popeza anakwezedwa ndi dzanja Lamanja la Mulungu, nalandira kwa Atate lonjezano la Mzimu Woyera, anatsanulira ici, cimene inu mupenya nimumva.

Macitidwe 2

Macitidwe 2:24-43