Macitidwe 2:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzali m'masiku otsiriza, anena Mulungu,Ndidzathira ca Mzimu wansa pa thupi liri lonse,Ndipo ana anu amuna, ndi akazi adzanenera,Ndipo anyamata anu adzaona masomphenya,Ndi akulu anu adzalota maloto;

Macitidwe 2

Macitidwe 2:16-22