Macitidwe 19:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene ena anaumitsa mtima ndi kusamvera, nanenera zoipa Njirayo pamaso pa anthu, anawacokera, napatutsa akuphunzira, nafotokozera masiku onse m'sukulu ya Turano.

Macitidwe 19

Macitidwe 19:7-10