Macitidwe 19:40-41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

40. Pakutinso palipo potiopsya kuti adzatineneza za cipolowe ca lero; popeza palibe cifukwa ca kufotokozera za cipiringu cimene.

41. Ndipo pamene ananena izi, anamasula msonkhano.

Macitidwe 19