Macitidwe 19:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muona ndi kumva, kuti si pa Efeso pokha, koma monga pa Asiya ponse, Paulo uyu akopa ndi kutembenutsa anthu ambiri, ndi kuti, Si milungu iyi imene ipangidwa ndi manja:

Macitidwe 19

Macitidwe 19:19-32