Macitidwe 19:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Ayuda enanso oyendayenda, oturutsa ziwanda, anadziyesa kuchula pa iwo amene anali ndi mizimu yoipa dzina la Ambuye Yesu, kuti, Ndikulumbirirani pa Yesu amene amlalika Paulo.

Macitidwe 19

Macitidwe 19:10-21