Macitidwe 18:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapeza Myuda wina dzina lace Akula, pfuko lace la ku Ponto, atacoka catsopano ku Italiya, pamodzi ndi mkazi wace Priskila, cifukwa Klaudiyo analamulira Ayuda onse acoke m'Roma; ndipo Pauloanadza kwa iwo:

Macitidwe 18

Macitidwe 18:1-10