Macitidwe 17:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza tsono tiri mbadwa za Mulungu, sitiyenera kulingalira kuti umulungu uli wofanafana ndi golidi, kapena siliva, kapena mwala, woloca ndi luso ndi zolingalira za anthu.

Macitidwe 17

Macitidwe 17:19-34