Macitidwe 17:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulungu amene analenga dziko lapansi ndi zonse ziri momwemo, Iyeyo, ndiye mwini kumwamba ndi dziko lapansi, sakhala m'nyumba zakacisi zomangidwa ndi manja;

Macitidwe 17

Macitidwe 17:23-25