Macitidwe 17:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akukonda nzeru ena a Epikureya ndi a Stoiki anatengana naye. Ena anati, ici ciani afuna kunena wobwetuka uyu? Ndipo ena, Anga wolalikira ziwanda zacilendo, cifukwa analalikira Yesu ndi kuuka kwa akufa.

Macitidwe 17

Macitidwe 17:11-26