Macitidwe 17:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iwo amene anaperekeza Paulo anadza naye kufikira ku Atene; ndipo polandira iwo lamulo la kwa Sila ndi Timoteo kuti afulumire kudza kwa iye ndi cangu conse, anacoka.

Macitidwe 17

Macitidwe 17:8-18