Macitidwe 17:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene Ayuda a ku Tesalonika anazindikira kuti mau a Mulungu analalikidwa ndi Paulo ku Bereyanso, anadza komwekonso, nautsa, nabvuta makamu.

Macitidwe 17

Macitidwe 17:7-14