Macitidwe 16:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacita cotero masiku ambiri. Koma Paulo anabvutika mtima ndithu, naceuka, nati kwa mzimuwo, Ndikulamulira iwe m'dzina la Yesu Kristu, turuka mwa iye. Ndipo unaturuka nthawi yomweyo.

Macitidwe 16

Macitidwe 16:11-23