Macitidwe 15:40-41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

40. Koma Paulo anasankha Sila, namuka, woikizidwa ndi abale ku cisomo ca Ambuye.

41. Ndipo iye anapita kupyola pa Suriya ndi Kilikiya, nakhazikitsa Mipingo.

Macitidwe 15