Macitidwe 15:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene anafika ku Yerusalemu, analandiridwa ndi Mpingo, ndi atumwi ndi akuru, ndipo anabwerezanso zonse zimene Mulungu anacita nao.

Macitidwe 15

Macitidwe 15:1-11