Macitidwe 15:39-41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

39. Ndipo panali kupsetsana mtima, kotero kuti analekana wina ndi mnzace; ndipo Bamaba anatenga Marko, nalowa n'ngalawa, nanka ku Kupro.

40. Koma Paulo anasankha Sila, namuka, woikizidwa ndi abale ku cisomo ca Ambuye.

41. Ndipo iye anapita kupyola pa Suriya ndi Kilikiya, nakhazikitsa Mipingo.

Macitidwe 15