Macitidwe 15:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza tamva kuti ena amene anaturuka mwa ife anakubvutani ndi mau, nasoceretsa mitima yanu; amenewo sitinawalamulira;

Macitidwe 15

Macitidwe 15:22-26