Macitidwe 15:12-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Ndipo khamu lonse linatonthola; ndipo anamvera Bamaba ndi Paulo alikubwerezanso zizindikiro ndi zozizwitsa zimene Mulungu anacita nao pa amitundu.

13. Pamene iwo anatonthola Yakobo anayankha, nati,Abale, mverani ine:

14. Sumeoni wabwereza kuti poyamba Mulungu anayang'anira amitundu, kuti atenge mwa iwo anthu a dzina lace.

Macitidwe 15