Macitidwe 14:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace anakhala nthawi yaikuru nanenetsa zolimba mtima mwa Ambuye, amene anacitira umboni mau a cisomo cace, napatsa zizindikiro ndi zozizwa kuti zicitidwe ndi manja ao.

Macitidwe 14

Macitidwe 14:1-13