Macitidwe 14:27-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Pamene anafika nasonkhanitsa Mpingo anabwerezanso zomwe Mulungu anacita nao, kuti anatsegulira amitundu pa khomo la cikhulupiriro.

28. Ndipo anakhala pamenepo ndi akuphunzira nthawi yaikuru.

Macitidwe 14