Macitidwe 14:24-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo anapitirira pa Pisidiya, nafika ku Pamfuliya. Ndipo atalankhula mau m'Perge, anatsikira ku Ataliya;