Macitidwe 14:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma wansembe wa Zeu wa kumaso kwa mudzi, anadza nazo ng'ombe ndi maluwa kuzipata, nafuna kupereka nsembe pamodzi ndi makamu.

Macitidwe 14

Macitidwe 14:11-17