Macitidwe 14:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo kunali pa Ikoniyo kuti analowa pamodzi m'sunagoge wa Ayuda, nalankhula kotero, kuti khamu lalikuru la Ayuda ndi Ahelene anakhulupira.

2. Koma Ayuda osamvefa anautsa mitima ya Ahelene kuti aipse abale athu.

Macitidwe 14