Macitidwe 13:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulungu wa anthu awa Israyeli anasankha makolo athu, nakweza anthuwo pakugonerera iwo m'dziko la Aigupto, ndipo ndi dzanja lokwezeka anawaturutsa iwo m'menemo.

Macitidwe 13

Macitidwe 13:12-27