Macitidwe 12:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene adamgwira, anamuika m'ndende, nampereka kwa magulu anai a alonda, lonse anai anai, amdikire iye; ndipo anafuna kumturutsa kudza naye kwa anthu atapita Paskha.

Macitidwe 12

Macitidwe 12:3-13