Macitidwe 12:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma m'mene adawatambasulira dzanja akhale cete, anawafotokozera umo, adamturutsira Ambuye m'ndende. Ndipo anati, Muwauze Yakobo ndi abale izi, Ndipo anaturuka napita kwina.

Macitidwe 12

Macitidwe 12:12-18