Macitidwe 12:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Petro atatsitsimuka, anati, Tsopano ndidziwa zoona, kuti Ambuye anatuma mngelo wace nandilanditsa ine m'dzanja la Herode, ndi ku cilingiriro conse ca anthu a Israyeli.

Macitidwe 12

Macitidwe 12:5-12