Macitidwe 11:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anyanamuka mmodzi wa iwo, dzina lace Agabo, nalosa mwa Mzimu, kuti padzakhala njala yaikulu pa dziko lonse lokhalamo anthu; ndiyo idadza masiku a Klaudiyo.

Macitidwe 11

Macitidwe 11:25-30