Macitidwe 11:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo iwotu, akubalalika cifukwa ca cisautsoco cidadza pa Stefano, anafikira ku Foinike, ndi Kupro, ndi Antiokeya, osalankhula mau kwa wina yense koma kwa Ayuda okha.

Macitidwe 11

Macitidwe 11:11-28