Macitidwe 10:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma m'mawa mwace, pokhala paulendo pao iwowa, m'mene anayandikira mudzi, Petro anakwera pachindwi kukapemphera, ngati pa ora lacisanu ndi cimodzi; ndipo anagwidwa njala, nafuna kudya;

Macitidwe 10

Macitidwe 10:6-18