Macitidwe 10:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinatumiza kwa inu osacedwa; ndipo mwacita bwino mwadza kuno, Cifukwa cace taonani tiri tonse pano pamaso pa Mulungu, kumva zonse Ambuye anakulamulirani.

Macitidwe 10

Macitidwe 10:26-42