Macitidwe 1:19-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. ndipo cinadziwika ndi onse akukhala ku Yerusalemu; kotero kuti m'manenedwe ao kadzikoka kanachedwa Akeldama, ndiko, kadziko ka mwazi.)

20. Pakuti kwalembedwa m'buku la Masalmo,Pogonera pace pakhale bwinja,Ndipo pasakhale munthu wogonapo;Ndipo uyang'aniro wace autenge wina.

21. Potero kuyenera kuti wina wa amunawo anatsatana nafe nthawi yonseyi Ambuye Yesu analowa naturuka mwa ife,

Macitidwe 1