Macitidwe 1:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amenenso anati, Amuna a ku Galileya, muimiranji ndi kuyang'ana kumwamba? Yesu amene walandiridwa kunka Kumwamba kucokera kwa inu, adzadza momwemo monga munamuona alinkupita Kumwamba.

Macitidwe 1

Macitidwe 1:5-12