Luka 9:57 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene iwo analikuyenda m'njira, munthu anati kwa iye, Ine ndidzakutsatani kumene kuli konse mukapitako.

Luka 9

Luka 9:56-62