Luka 9:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu anayankha, nati, Ha! obadwa inu osakhulupirira ndi amphulupulu, ndidzakhala ndi inu nthawi yanji, ndi kulekerera inu? idza naye kuno mwana wako.

Luka 9

Luka 9:35-44