Luka 9:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo onani, umamgwira iye mzimu, napfuula modzidzimuka; ndipo umamng'amba iye ndi kumcititsa thobvu pakamwa, nucoka pa iye mwa unyenzi, numgola iye.

Luka 9

Luka 9:34-42