Luka 9:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Petro ndi iwo anali naye analemedwa ndi tulo; koma m'mene anayera m'maso ndithu, anaona ulemerero wace, ndi amuna awiriwo akuimirira ndi iye.

Luka 9

Luka 9:29-40