Luka 9:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene padatha ngati masiku asanu ndi atatu atanena mau amenewa, Iye anatenga Petro ndi Yohane ndi Yakobo apite naye, nakwera m'phiri kukapemphera.

Luka 9

Luka 9:21-31