Luka 9:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anayankha nati, Yohane Mbatizi; koma ena, Eliya; ndi ena, kuti anauka mmodzi wa aneneri akale.

Luka 9

Luka 9:10-27