Luka 9:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma unyinji wa anthu, pamene anadziwa, anamtsata Iye; ndipo iye anawalandira, nalankhula nao za Ufumu wa Mulungu, naciritsa amene anasowa kuciritsidwa.

Luka 9

Luka 9:8-16