Luka 8:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu anati, Wandikhudza Ine ndani? Koma pamene onse anakana, Petro ndi iwo akukhala naye anati, Ambuye, anthu aunyinji alikukankhana pa Inu ndi kukanikizana.

Luka 8

Luka 8:36-54