Luka 8:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu aunyinji onse a dziko la Agerasa Ioyandikira anamfunsa iye acoke kwa iwo; cifukwa anagwidwa ndi mantha akuru. Ndipo iye analowa m'ngalawa, nabwerera.

Luka 8

Luka 8:32-47