Luka 8:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ziwandazo zinaturuka mwa munthu nizilowa mu nkhumba: ndipo gululo linatsika liwiro potsetsereka ndi kulowa m'nyanjamo, nilitsamwa.

Luka 8

Luka 8:28-38