Luka 7:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Mfarisi, amene adamuitana iye, pakuona, ananena mwa yekha, nati, Akadakhala mneneri uyu akadazindikira ali yani, ndi wotani mkaziyo womkhudza iye, cifukwa ali wocimwa.

Luka 7

Luka 7:36-44