Luka 7:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yohane anaitana awiri a ophunzira ace, nawatuma kwa Ambuye, nanena, Kodi ndinu wakudzayo, kapena tiyang'anire wina?

Luka 7

Luka 7:16-21