Luka 6:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti analowa m'nyumba ya Mulungu, natenga mikate yoonetsera, nadya, napatsanso iwo anali naye pamodzi; imeneyi yosaloledwa kudya ena koma ansembe okha?

Luka 6

Luka 6:1-12