Luka 6:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Odala inu, pamene anthu adzada inu, nadzapatula inu, nadzatonza inu, nadzalitaya dzina lanu monga loipa, cifukwa ca Mwana wa munthu.

Luka 6

Luka 6:14-28